Nehemiya 3:19 BL92

19 Ndi pa mbali pace Ezeri mwana wa Yesuwa, mkuru wa Mizipa, anakonza gawo lina, pandunji pokwerera ku nyumba yosungamo zida za nkhondo, popindirira linga.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 3

Onani Nehemiya 3:19 nkhani