Nehemiya 3:3 BL92

3 Ndi cipata cansomba anacimanga ana a Hasenaa; anamanga mitanda yace, ndi kuika zitseko zace, zokowera zace, ndi mipingiridzo yace.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 3

Onani Nehemiya 3:3 nkhani