Nehemiya 4:1 BL92

1 Ndipo kunali, atamva Sanibalati kuti tinalikumanga lingali, kudamuipira, nakwiya kwakukuru, naseka Ayuda pwepwete.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 4

Onani Nehemiya 4:1 nkhani