Nehemiya 4:10 BL92

10 Ndipo Ayuda anati, Mphamvu ya osenza akatundu yatha, ndi dothi licuruka, motero sitidzakhoza kumanga lingali.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 4

Onani Nehemiya 4:10 nkhani