Nehemiya 4:21 BL92

21 Momwemo tinalikugwira nchito; gawo lina la iwo linagwira nthungo kuyambira mbanda kuca mpaka zaturuka nyenyezi.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 4

Onani Nehemiya 4:21 nkhani