Nehemiya 4:5 BL92

5 ndipo musakwirira mphulupulu yao, ndi kulakwa kwao kusafafanizike pamaso panu; pakuti anautsa mkwiyo wanu pamaso pa omanga linga.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 4

Onani Nehemiya 4:5 nkhani