15 Ndipo linga linatsirizika pa tsiku la makumi awiri ndi lacisanu la mwezi wa Eluli, titalimanga masiku makumi asanu mphambu awiri.
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 6
Onani Nehemiya 6:15 nkhani