19 Anachulanso nchito zace zokoma pamaso panga namfotokozera iye mau anga. Ndipo Tobiya anatumiza akalata kuti andiopse ine.
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 6
Onani Nehemiya 6:19 nkhani