Nehemiya 7:64 BL92

64 Awa anafunafuna maina ao m'buku la iwo owerengedwa mwa cibadwidwe, koma osawapeza; potero anawayesa odetsedwa, nawacotsa ku nchito ya nsembe.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 7

Onani Nehemiya 7:64 nkhani