2 Ndipo Ezara wansembe anabwera naco cilamulo pamaso pa msonkhano, ndiwo amuna ndi akazi, ndi yense wakumva ndi kuzindikira tsiku loyamba la mwezi wacisanu ndi ciwiri.
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 8
Onani Nehemiya 8:2 nkhani