5 Ndipo Ezara anafunyulula bukulo pamaso pa anthu onse, popeza iye anasomphokera anthu onse; ndipo polifunyulula anthu onse ananyamuka.
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 8
Onani Nehemiya 8:5 nkhani