21 Ndipo munawalera zaka makumi anai m'cipululu, osasowa kanthu iwo; zobvala zao sizinatha, ndi mapazi ao sanatupa.
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 9
Onani Nehemiya 9:21 nkhani