Nehemiya 9:23 BL92

23 Ana aonso munawacurukitsa monga nyenyezi za m'mwamba, nimunawalowetsa m'dziko mudalinena kwa makolo ao, alowemo likhale lao lao.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 9

Onani Nehemiya 9:23 nkhani