26 Koma anakhala osamvera, napandukira Inu, nataya cilamulo canu m'mbuyo mwao napha aneneri anu akuwacitira umboni, kuwabwezera kwa Inu, nacita zopeputsa zazikuru.
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 9
Onani Nehemiya 9:26 nkhani