34 ndi mafumu athu, akuru athu, ansembe athu, ndi makolo athu, sanasunga cilamulo canu, kapena kumvera malamulo anu, ndi mboni zanu, zimene munawacitira umboni nazo.
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 9
Onani Nehemiya 9:34 nkhani