Nehemiya 9:4 BL92

4 Pamenepo anaimirira pa ciunda ca Alevi Yesuwa, ndi Bani, Kadimiyeli, Sebaniya, Buni, Serebiya, Bani, ndi Kenani, napfuula ndi mau akuru kwa Yehova Mulungu wao.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 9

Onani Nehemiya 9:4 nkhani