2 Akorinto 1:1 BL92

1 PAULO, mtumwi wa Kristu Yesu, mwa cifuniro ca Mulungu, ndi Timoteo mbaleyo, kwa Mpingo wa Mulungu umene uli ku Korinto, pamodzi ndi oyera mtima onse amene ali m'Akaya lonse:

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 1

Onani 2 Akorinto 1:1 nkhani