14 monganso munatibvomerezera ife pena, kuti ife ndife kudzitamandira kwanu, monga momwe inunso muli kudzitamandira kwathu m'tsiku la Ambuye wathu Yesu.
Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 1
Onani 2 Akorinto 1:14 nkhani