2 Akorinto 1:4 BL92

4 woo titonthoza ife m'nsautso yathu yonse, kuti tidzathe ife kutonthoza iwo okhala m'nsautso iri yonse, mwa citonthozo cimene titonthozedwa naco tokha ndi Mulungu.

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 1

Onani 2 Akorinto 1:4 nkhani