2 Akorinto 11:15 BL92

15 Cifukwa cace sikuli kanthu kwakukuru ngatinso atumiki ace adzionetsa monga atumiki a cilungamo; amene cimariziro cao cidzakhala monga nchito zao.

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 11

Onani 2 Akorinto 11:15 nkhani