20 Pakuti mulola ngati wina akuyesani inu akapolo, ngati wina alikwira inu, ngati wina alanda zanu, ngati wina adzikuza, ngati wina akupandani pankhope.
Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 11
Onani 2 Akorinto 11:20 nkhani