23 Kodi ali atumiki a Kristu? (ndilankhula monga moyaruka), makamaka ine; m'zibvutitso mocurukira, m'ndende mocurukira, m'mikwingwirima mosawerengeka, muimfa kawiri kawiri.
Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 11
Onani 2 Akorinto 11:23 nkhani