11 Cotsalira, abale, kondwerani, Mucitidwe angwiro; mutorithozedwe; khalani a mtima umodzi, khalani mumtendere; ndipo Mulungu wa cikondi ndi mtendere akhale pamodzi ndi inu.
Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 13
Onani 2 Akorinto 13:11 nkhani