2 Akorinto 13:4 BL92

4 pakuti anapacikidwa m'ufoko, koma ali ndi moyo mu mphamvu ya Mulungu. Pakuti ifenso tiri ofok a mwa iye, koma tidzakhala ndi moyo pamodzi ndi iye, mu mphamvu ya Mulungu, ya kwa inu.

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 13

Onani 2 Akorinto 13:4 nkhani