2 Akorinto 13:7 BL92

7 Ndipo tipemphera Mulungu kuti musacite kanthu koipa; sikuti ife tikaoneke obvomerezeka, koma kuti inu mukacite cabwino, tingakhale ife tikhala monga osatsimikizidwa.

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 13

Onani 2 Akorinto 13:7 nkhani