17 Pakuti sitikhala monga ambiriwo, akucita malonda nao mau a Mulungu; koma monga mwa coona mtima, koma monga mwa Mulungu pamaso pa Mulungu, tilankhula mwa Kristu.
Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 2
Onani 2 Akorinto 2:17 nkhani