4 Pakuti m'cisautso cambiri ndi kuwawa mtima ndinalembera inu ndi misozi yambiri; si kuti ndikumvetseni cisoni, koma kuti mukadziwe cikondi ca kwa inu, cimene ndiri naco koposa.
Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 2
Onani 2 Akorinto 2:4 nkhani