9 monga osadziwika, angakhale adziwika bwino; monga alinkufa, ndipo taonani, tiri ndi moyo; monga olangika, ndipo osaphedwa;
Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 6
Onani 2 Akorinto 6:9 nkhani