1 Pokhala nao tsono malonjezano amenewa, okondedwa, tidzikonzere tokha kuleka codetsa conse ca thupi ndi ca mzimu, ndi kutsirfza ciyero m'kuopa Mulungu.
Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 7
Onani 2 Akorinto 7:1 nkhani