Danieli 2:40 BL92

40 Ndi ufumu wacinai udzakhala wolimba ngati citsulo, popeza citsulo ciphwanya ndi kufoketsa zonse; ndipo monga citsulo ciswa zonsezi, uwu udzaphwanya ndi kuswa.

Werengani mutu wathunthu Danieli 2

Onani Danieli 2:40 nkhani