25 Pamenepo mfumu Dariyo analembera kwa anthu, mitundu ya anthu, ndi a manenedwe onse okhala pa dziko lonse lapansi, Mtendere ucurukire inu.
Werengani mutu wathunthu Danieli 6
Onani Danieli 6:25 nkhani