4 Ndipo kunali, pakumva'mau awa, ndinakhala pansi ndi kulira misozi, ndi kucita maliro masiku ena, ndinasalanso, ndi kupemphera pamaso pa Mulungu wa Kumwamba,
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 1
Onani Nehemiya 1:4 nkhani