Nehemiya 12:31 BL92

31 Pamenepo ndinakwera nao akuru a Yuda pa lingali, ndinaikanso oyamikira magulu awiri akuru oyenda molongosoka; lina loyenda ku dzanja lamanja palinga kumka ku cipata ca kudzala;

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 12

Onani Nehemiya 12:31 nkhani