16 Koma olamulira sanadziwa uko ndinamuka, kapena cocita ine; sindidauzenso kufikira pamenepo Ayuda, kapena ansembe, kapena aufuru, kapena olamulira, kapena otsala akucita nchitoyi.
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 2
Onani Nehemiya 2:16 nkhani