17 Pamenepo ndinanena nao, Muona coipa m'mene tirimo, kuti Yerusalemu ali bwinja, ndi zipata zace zotentha ndi moto; tiyeni, timange linga la Yerusalemu, tisakhalenso cotonzedwa.
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 2
Onani Nehemiya 2:17 nkhani