18 Ndinawauzanso za dzanja la Mulungu wanga londikhalira mokoma, ndiponso za mau anandiuza mfumu. Nati iwo, Tinyamuke, timange. Cotero anandilimbitsira manja mokoma.
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 2
Onani Nehemiya 2:18 nkhani