19 Koma Sanibalati Mhoroni, ndi Tobiya kapolo M-amoniyo, ndi Gesemu M-arabu, anamva natiseka pwepwete, natipeputsa, nati, Ciani ici mucicita? Mulikupandukira mfumu kodi?
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 2
Onani Nehemiya 2:19 nkhani