Nehemiya 2:6 BL92

6 Ninena nane mfumu, irikukhala pansi pamodzi ndi mkazi wace wamkuru, Ulendo wako ngwa nthawi yanji, udzabweranso liti? Ndipo kudakonda mfumu kunditumiza nditaichula nthawi.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 2

Onani Nehemiya 2:6 nkhani