7 Ndinanenanso kwa mfumu, Cikakomera mfumu, indipatse akalata kwa ziwanga za tsidya lija la mtsinje, andilole ndipitirire mpaka ndifikira ku Yuda;
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 2
Onani Nehemiya 2:7 nkhani