Nehemiya 7:39 BL92

39 Ansembe: ana a Yedaya, a nyumba ya Yesuwa, mazana asanu ndi anai mphambu makumi asanu ndi awiri kudza atatu.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 7

Onani Nehemiya 7:39 nkhani