Nehemiya 7:69 BL92

69 ngamira zao mazana anai mphambu makumi atatu kudza asanu aburu ao zikwi zisanu ndi cimodzi mphambu mazana asanu ndi awiri kudza makumi awiri.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 7

Onani Nehemiya 7:69 nkhani