70 Ndipo ena a akuru a nyumba za makolo anapereka kunchito. Kazembeyo anapereka kucuma madariki agolidi cikwi cimodzi, mbale zawazira makumi asanu, maraya a ansembe makumi atatu.
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 7
Onani Nehemiya 7:70 nkhani