Nehemiya 7:71 BL92

71 Enanso a akuru a nyumba za makolo anapereka ku cuma ca nchitoyi, madariki agolidi zikwi makumi awiri, ndi miyeso ya siliva zikwi ziwiri mphambu mazana awiri.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 7

Onani Nehemiya 7:71 nkhani