Nehemiya 7:72 BL92

72 Zopereka za anthu otsala ndizo madariki agolidi zikwi makumi awiri, ndi miyeso ya siliva zikwi ziwiri, ndi maraya a ansembe makumi asanu ndi limodzi mphambu asanu ndi awiri.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 7

Onani Nehemiya 7:72 nkhani