11 Ndipo Alevi anatontholetsa anthu onse, ndi kuti, Khalani muli cete; pakuti lero ndi lopatulika; musamacita cisoni.
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 8
Onani Nehemiya 8:11 nkhani