12 Napita anthu onse kudya ndi kumwa, ndi kutumiza magawo, ndi kusekerera kwakukuru; popeza anazindikira mau amene adawafotokozera.
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 8
Onani Nehemiya 8:12 nkhani