13 Ndipo m'mawa mwace akuru a nyumba za makolo a anthu onse, ansembe, ndi Alevi anasonkhana pamodzi kwa Ezara mlembi, kuti atole nzeru za mau a cilamulo.
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 8
Onani Nehemiya 8:13 nkhani