2 Nadzipatula a mbumba ya Israyeli kwa alendo onse, naimirira, naulula zocimwa zao, ndi mphulupulu za makolo ao.
Werengani mutu wathunthu Nehemiya 9
Onani Nehemiya 9:2 nkhani