21 Pakuti popeza m'nzeru ya Mulungu dziko lapansi, mwa nzeru yace, silinadziwa Mulungu, cidamkonda Mulungu kupulumutsa okhulupirawo mwa copusa ca kulalikira.
Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 1
Onani 1 Akorinto 1:21 nkhani