1 Akorinto 11:22 BL92

22 Nanga mulibe nyumba za kudyeramo ndi kumweramo? Kapena kodi munyoza Eklesia wa Mulungu, ndi kunyoza iwo amene alibe kanthu? Ndidzanena ciani kwa inu? Kodi ndidzatama inu m'menemo? Sindikutamani.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 11

Onani 1 Akorinto 11:22 nkhani